Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Panali pa nthawi imeneyi pamene ntchito yomanga nyumba ya Mulungu, imene inali ku Yerusalemu, inaima ndipo inakhala chiimire mpaka chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo+ mfumu ya Perisiya.

  • Ezara 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma maso+ a Mulungu wawo anali+ pa akulu a Ayuda, ndipo anthu aja sanawasiyitse ntchitoyo. Anadikira mpaka pamene analemba chikalata chokhudza nkhaniyo n’kuchitumiza kwa Dariyo, ndiponso mpaka pamene chikalata choyankha nkhani imeneyi chinabwera.

  • Ezara 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Panali pa nthawi imeneyi pamene mfumu Dariyo inaika lamulo loti afufuze ndipo anafufuza m’nyumba yosungiramo mabuku ofotokoza mbiri yakale,+ momwe analinso kusungiramo zinthu zamtengo wapatali zimene zinaikidwa ku Babuloko.

  • Danieli 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano ndikufotokozera choonadi:+

      “Mu ufumu wa Perisiya+ mudzauka mafumu atatu, ndipo mfumu yachinayi+ idzasonkhanitsa chuma chambiri kuposa ena onsewa.+ Ndipo ikadzangokhala yamphamvu chifukwa cha chuma chakecho idzaukira ufumu wa Girisi ndi mphamvu zake zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena