-
2 Mafumu 17:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Chotero mfumu ya Asuri inalandira uthenga wakuti: “Mitundu imene munaichotsa kwawo n’kukaikhazika m’mizinda ya ku Samariya, sikudziwa chipembedzo cha Mulungu wa m’dzikolo, moti iye wakhala akutumiza mikango pakati pawo+ imene ikuwapha, popeza palibe amene akudziwa chipembedzo cha Mulungu wa m’dzikolo.”
-