Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 36:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 M’chaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya,+ Yehova analimbikitsa mtima+ wa Koresi mfumu ya Perisiya kuti mawu a Yehova+ kudzera mwa Yeremiya+ akwaniritsidwe. Pamenepo Koresiyo anatumiza mawu amene analengezedwa mu ufumu wake wonse. Mawuwo analembedwanso m’makalata,+ kuti:

  • Ezara 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 M’chaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya, Yehova analimbikitsa+ mtima wa Koresi mfumu ya Perisiya kuti mawu a Yehova kudzera mwa Yeremiya+ akwaniritsidwe. Pamenepo Koresiyo anatumiza mawu amene analengezedwa+ mu ufumu wake wonse. Mawuwo analembedwanso m’makalata,+ kuti:

  • Ezara 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Komabe m’chaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Babulo, mfumu Koresi inaika lamulo loti nyumba ya Mulunguyi imangidwenso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena