Ezara 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Izi n’zimene zinali m’kalata+ imene Tatenai+ bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzake,+ ndiponso abwanamkubwa aang’ono amene anali kutsidya lina la Mtsinje, anatumiza kwa mfumu Dariyo. Ezara 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzawo anachita mogwirizana ndi mawu amene mfumu Dariyo inatumiza. Anachita zimenezi mwamsanga.
6 Izi n’zimene zinali m’kalata+ imene Tatenai+ bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzake,+ ndiponso abwanamkubwa aang’ono amene anali kutsidya lina la Mtsinje, anatumiza kwa mfumu Dariyo.
13 Kenako Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzawo anachita mogwirizana ndi mawu amene mfumu Dariyo inatumiza. Anachita zimenezi mwamsanga.