Ezara 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno ndinawasonkhanitsa pamtsinje+ umene umafika ku Ahava+ ndipo tinamanga msasa pamenepo n’kukhalapo masiku atatu kuti ndiwaonetsetse anthuwo+ ndi ansembe,+ koma sindinapezepo ana a Levi.+
15 Ndiyeno ndinawasonkhanitsa pamtsinje+ umene umafika ku Ahava+ ndipo tinamanga msasa pamenepo n’kukhalapo masiku atatu kuti ndiwaonetsetse anthuwo+ ndi ansembe,+ koma sindinapezepo ana a Levi.+