Ezara 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho ena mwa ana a Isiraeli, ansembe,+ Alevi,+ oimba,+ alonda a pazipata,+ ndi Anetini+ anapita ku Yerusalemu m’chaka cha 7 cha mfumu Aritasasita.+
7 Choncho ena mwa ana a Isiraeli, ansembe,+ Alevi,+ oimba,+ alonda a pazipata,+ ndi Anetini+ anapita ku Yerusalemu m’chaka cha 7 cha mfumu Aritasasita.+