Ezara 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa ana a Pahati-mowabu+ panali Eliho-enai mwana wa Zerahiya. Iye anali ndi amuna 200. Ezara 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa ana a Pahati-mowabu+ panali Adena, Kelali, Benaya, Maaseya, Mataniya, Bezaleli, Binui ndi Manase. Nehemiya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malikiya mwana wamwamuna wa Harimu,+ komanso Hasubu mwana wamwamuna wa Pahati-mowabu,+ anakonza gawo lina la mpandawo, ndipo anakonzanso Nsanja ya Mauvuni.+ Nehemiya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ana a Pahati-mowabu,+ ochokera mwa ana a Yesuwa ndi Yowabu,+ 2,818. Nehemiya 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atsogoleri awa a anthu anatsimikiziranso panganoli: Parosi, Pahati-mowabu,+ Elamu, Zatu, Bani,
30 Pa ana a Pahati-mowabu+ panali Adena, Kelali, Benaya, Maaseya, Mataniya, Bezaleli, Binui ndi Manase.
11 Malikiya mwana wamwamuna wa Harimu,+ komanso Hasubu mwana wamwamuna wa Pahati-mowabu,+ anakonza gawo lina la mpandawo, ndipo anakonzanso Nsanja ya Mauvuni.+