Ezara 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Pahati-mowabu,+ ochokera mwa ana a Yesuwa ndi Yowabu,+ 2,812. Nehemiya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malikiya mwana wamwamuna wa Harimu,+ komanso Hasubu mwana wamwamuna wa Pahati-mowabu,+ anakonza gawo lina la mpandawo, ndipo anakonzanso Nsanja ya Mauvuni.+ Nehemiya 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atsogoleri awa a anthu anatsimikiziranso panganoli: Parosi, Pahati-mowabu,+ Elamu, Zatu, Bani,
11 Malikiya mwana wamwamuna wa Harimu,+ komanso Hasubu mwana wamwamuna wa Pahati-mowabu,+ anakonza gawo lina la mpandawo, ndipo anakonzanso Nsanja ya Mauvuni.+