Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Ezara 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Muziwapatsa zimenezi kuti nthawi zonse+ azipereka nsembe zoziziritsa mtima+ kwa Mulungu wakumwamba, ndiponso kuti azipempherera moyo wa mfumu ndi ana ake.+ Yesaya 60:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti mtundu uliwonse ndi ufumu uliwonse umene sudzakutumikira udzawonongedwa, ndipo mitundu ya anthu idzasakazidwa ndithu.+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
10 Muziwapatsa zimenezi kuti nthawi zonse+ azipereka nsembe zoziziritsa mtima+ kwa Mulungu wakumwamba, ndiponso kuti azipempherera moyo wa mfumu ndi ana ake.+
12 Pakuti mtundu uliwonse ndi ufumu uliwonse umene sudzakutumikira udzawonongedwa, ndipo mitundu ya anthu idzasakazidwa ndithu.+