Ezara 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zonse zimene Mulungu wakumwamba+ walamula+ zokhudza nyumba yake, zichitike modzipereka kwambiri+ kuti mkwiyo usayakire dziko la mfumu ndiponso usayakire ana ake.+ Yeremiya 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso mzinda umene ndakuchititsani kukhalamo monga akapolo, muziufunira mtendere. Muziupempherera kwa Yehova, pakuti mzindawo ukakhala pa mtendere inunso mudzakhala pa mtendere.+ 1 Timoteyo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muchite zimenezi m’malo mwa mafumu+ ndi m’malo mwa anthu onse apamwamba,+ kuti tikhale ndi moyo wabata ndi wamtendere, ndiponso kuti tikhale odzipereka kwa Mulungu mokwanira komanso tikhale oganiza bwino.+
23 Zonse zimene Mulungu wakumwamba+ walamula+ zokhudza nyumba yake, zichitike modzipereka kwambiri+ kuti mkwiyo usayakire dziko la mfumu ndiponso usayakire ana ake.+
7 Komanso mzinda umene ndakuchititsani kukhalamo monga akapolo, muziufunira mtendere. Muziupempherera kwa Yehova, pakuti mzindawo ukakhala pa mtendere inunso mudzakhala pa mtendere.+
2 Muchite zimenezi m’malo mwa mafumu+ ndi m’malo mwa anthu onse apamwamba,+ kuti tikhale ndi moyo wabata ndi wamtendere, ndiponso kuti tikhale odzipereka kwa Mulungu mokwanira komanso tikhale oganiza bwino.+