Ezara 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Khalani maso ndipo khalani atcheru mpaka mukaziyeze+ pamaso pa atsogoleri a ansembe, atsogoleri a Alevi ndi pamaso pa akalonga a makolo a Aisiraeli ku Yerusalemu, m’zipinda zodyera+ za panyumba ya Yehova.”
29 Khalani maso ndipo khalani atcheru mpaka mukaziyeze+ pamaso pa atsogoleri a ansembe, atsogoleri a Alevi ndi pamaso pa akalonga a makolo a Aisiraeli ku Yerusalemu, m’zipinda zodyera+ za panyumba ya Yehova.”