Deuteronomo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova Mulungu wanu adzabweza kwawo anthu a mtundu wanu amene anagwidwa ndi kupita kudziko lina,+ ndipo adzakumverani chifundo+ n’kukusonkhanitsaninso pamodzi kuchokera pakati pa anthu onse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.+ 2 Mbiri 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuwonjezera apo, Nebukadinezara anagwira anthu amene sanaphedwe ndi lupanga ndipo anawatenga kupita nawo ku Babulo.+ Anthuwo anakakhala antchito+ ake ndi a ana ake kufikira pamene ufumu wa Perisiya+ unayamba kulamulira.
3 Yehova Mulungu wanu adzabweza kwawo anthu a mtundu wanu amene anagwidwa ndi kupita kudziko lina,+ ndipo adzakumverani chifundo+ n’kukusonkhanitsaninso pamodzi kuchokera pakati pa anthu onse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.+
20 Kuwonjezera apo, Nebukadinezara anagwira anthu amene sanaphedwe ndi lupanga ndipo anawatenga kupita nawo ku Babulo.+ Anthuwo anakakhala antchito+ ake ndi a ana ake kufikira pamene ufumu wa Perisiya+ unayamba kulamulira.