Deuteronomo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+ Nehemiya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho atangomva chilamulocho,+ anayamba kupatula+ khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana kuwachotsa pakati pa Isiraeli. 2 Akorinto 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Choncho tulukani pakati pawo, lekanani nawo,’ watero Yehova.* ‘Musakhudze chinthu chodetsedwa,’”+ “‘ndipo ndidzakulandirani.’”+
3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+
3 Choncho atangomva chilamulocho,+ anayamba kupatula+ khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana kuwachotsa pakati pa Isiraeli.
17 “‘Choncho tulukani pakati pawo, lekanani nawo,’ watero Yehova.* ‘Musakhudze chinthu chodetsedwa,’”+ “‘ndipo ndidzakulandirani.’”+