Nehemiya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Alevi anali kufotokozera anthu chilamulocho,+ anthuwo ataimirira.+ Alevi amenewo anali Yesuwa, Bani, Serebiya,+ Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi,+ Hanani ndi Pelaya.+ Nehemiya 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Panalinso Sabetai+ ndi Yozabadi,+ mwa atsogoleri a Alevi. Amenewa anali kuyang’anira ntchito ya panja pa nyumba ya Mulungu woona.
7 Pamenepo Alevi anali kufotokozera anthu chilamulocho,+ anthuwo ataimirira.+ Alevi amenewo anali Yesuwa, Bani, Serebiya,+ Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi,+ Hanani ndi Pelaya.+
16 Panalinso Sabetai+ ndi Yozabadi,+ mwa atsogoleri a Alevi. Amenewa anali kuyang’anira ntchito ya panja pa nyumba ya Mulungu woona.