Levitiko 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.” Deuteronomo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+
11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.”
10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+