Ezara 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anauza anthu kuti alengeze mu Yuda ndi Yerusalemu yense kwa anthu onse amene anachokera ku ukapolo+ kuti asonkhane ku Yerusalemu,
7 Kenako anauza anthu kuti alengeze mu Yuda ndi Yerusalemu yense kwa anthu onse amene anachokera ku ukapolo+ kuti asonkhane ku Yerusalemu,