Ezara 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano nawa mayina a atsogoleri a nyumba za makolo awo,+ ndi mndandanda wa mayina wotsatira makolo+ a anthu amene anachoka nane ku Babulo, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita:+
8 Tsopano nawa mayina a atsogoleri a nyumba za makolo awo,+ ndi mndandanda wa mayina wotsatira makolo+ a anthu amene anachoka nane ku Babulo, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita:+