Esitere 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo anatenga Esitere kupita naye kwa Mfumu Ahasiwero, kunyumba yake yachifumu, m’mwezi wa 10 umene ndi mwezi wa Tebeti,* m’chaka cha 7+ cha ulamuliro wa Mfumu Ahasiwero.
16 Pamenepo anatenga Esitere kupita naye kwa Mfumu Ahasiwero, kunyumba yake yachifumu, m’mwezi wa 10 umene ndi mwezi wa Tebeti,* m’chaka cha 7+ cha ulamuliro wa Mfumu Ahasiwero.