Esitere 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando+ akalonga ndi atumiki ake onse, akuluakulu a asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka+ ndi akalonga a m’zigawo za ufumu wake.+
3 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando+ akalonga ndi atumiki ake onse, akuluakulu a asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka+ ndi akalonga a m’zigawo za ufumu wake.+