Levitiko 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Munthu akachimwa mwa kuchita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite, ngakhale kuti anachita mosazindikira,+ komabe wapalamula mlandu, pamenepo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.+ Levitiko 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 iye akachimwa mwa njira imeneyi, ndipo wapalamuladi,+ azibweza zinthu zimene anafwambazo, kapena zinthu zimene analanda mwachinyengo, kapena chimene chili m’manja mwake chimene anam’sungitsa, kapena chinthu chotayika chimene anatola,
17 “Munthu akachimwa mwa kuchita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite, ngakhale kuti anachita mosazindikira,+ komabe wapalamula mlandu, pamenepo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.+
4 iye akachimwa mwa njira imeneyi, ndipo wapalamuladi,+ azibweza zinthu zimene anafwambazo, kapena zinthu zimene analanda mwachinyengo, kapena chimene chili m’manja mwake chimene anam’sungitsa, kapena chinthu chotayika chimene anatola,