Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Aa, Yehova. Chonde, tcherani khutu ku pemphero la ine mtumiki wanu ndiponso pemphero+ la atumiki anu amene amasangalala ndi kuopa dzina lanu.+ Chonde, ndithandizeni ine mtumiki wanu kuti zinthu zindiyendere bwino lero+ ndipo mwamunayu andimvere chisoni.”+

      Pa nthawi imeneyi, ine ndinali woperekera chikho+ kwa mfumu.

  • Nehemiya 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chinanso: Kwa zaka 12, kuchokera tsiku limene anandiika kukhala bwanamkubwa wawo+ m’dziko la Yuda, m’chaka cha 20+ mpaka m’chaka cha 32+ cha mfumu Aritasasita,+ ine ndi abale anga sitinadye chakudya choyenera kuperekedwa kwa bwanamkubwa.+

  • Nehemiya 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano amene anatsimikizira panganoli ndi chidindo+ chawo ndi awa:

      Nehemiya+ amene ndiye Tirisata,+ mwana wa Hakaliya,+

      Komanso Zedekiya,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena