Nehemiya 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 kutinso tisapereke ana athu aakazi kwa mitundu ya anthu ya m’dzikoli, ndiponso tisatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana athu aamuna.+
30 kutinso tisapereke ana athu aakazi kwa mitundu ya anthu ya m’dzikoli, ndiponso tisatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana athu aamuna.+