Nehemiya 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pake ndinafika kwa abwanamkubwa+ kutsidya lina la Mtsinje ndi kuwapatsa makalata a mfumu. Kuwonjezera apo, mfumu inandipatsa akuluakulu a gulu lankhondo ndi asilikali okwera pamahatchi* kuti ndiyende nawo.
9 Pambuyo pake ndinafika kwa abwanamkubwa+ kutsidya lina la Mtsinje ndi kuwapatsa makalata a mfumu. Kuwonjezera apo, mfumu inandipatsa akuluakulu a gulu lankhondo ndi asilikali okwera pamahatchi* kuti ndiyende nawo.