Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kenako, Benjamini ndi Hasubu anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yawo kuchokera pamene ansembe analekezera. Kenako, Azariya mwana wamwamuna wa Maaseya, mwana wamwamuna wa Ananiya, anakonza mpandawo pafupi ndi nyumba yake kuchokera pamene Benjamini ndi Hasubu analekezera.

  • Nehemiya 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ansembe anakonza mpandawo kuyambira kumtunda kwa Chipata cha Hatchi,+ ndipo aliyense anali kukonza patsogolo pa nyumba yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena