2 Mbiri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha+ ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.+ Ezara 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako ndinalamula kuti tisale kudya tili kumtsinje wa Ahava kuja, kuti tidzichepetse+ pamaso pa Mulungu wathu ndi kumupempha kuti atisonyeze njira yoyenera+ kwa ife, ana athu,+ ndi katundu wathu yense. Salimo 69:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo ndinalira ndi kusala kudya chifukwa cha moyo wanga,+Koma anthu anali kungonditonza chifukwa cha zimenezo.+
3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha+ ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.+
21 Kenako ndinalamula kuti tisale kudya tili kumtsinje wa Ahava kuja, kuti tidzichepetse+ pamaso pa Mulungu wathu ndi kumupempha kuti atisonyeze njira yoyenera+ kwa ife, ana athu,+ ndi katundu wathu yense.
10 Ndipo ndinalira ndi kusala kudya chifukwa cha moyo wanga,+Koma anthu anali kungonditonza chifukwa cha zimenezo.+