Nehemiya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Atekowa+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Zadoki analekezera. Koma anthu otchuka pakati pa Atekowa+ sanagonjere ambuye awo ndi kuwatumikira.
5 Ndiyeno Atekowa+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Zadoki analekezera. Koma anthu otchuka pakati pa Atekowa+ sanagonjere ambuye awo ndi kuwatumikira.