1 Mbiri 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kufikira nthawi imeneyo, iye anali kukhala pachipata cha mfumu+ kum’mawa. Amenewa anali alonda a pazipata za misasa ya ana a Levi.+ 1 Mbiri 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Maere a kum’mawa anagwera Selemiya.+ Anachitanso maere a Zekariya+ mwana wake, yemwe anali phungu+ wanzeru, ndipo maere ake anali oti akhale kumpoto.+ 2 Mbiri 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kore mwana wa Imuna Mlevi anali mlonda wa pachipata+ chakum’mawa+ amene anali kuyang’anira zopereka zaufulu+ zopita kwa Mulungu woona ndi kugawa zopereka za Yehova+ ndi zinthu zopatulika koposa.+
18 Kufikira nthawi imeneyo, iye anali kukhala pachipata cha mfumu+ kum’mawa. Amenewa anali alonda a pazipata za misasa ya ana a Levi.+
14 Maere a kum’mawa anagwera Selemiya.+ Anachitanso maere a Zekariya+ mwana wake, yemwe anali phungu+ wanzeru, ndipo maere ake anali oti akhale kumpoto.+
14 Kore mwana wa Imuna Mlevi anali mlonda wa pachipata+ chakum’mawa+ amene anali kuyang’anira zopereka zaufulu+ zopita kwa Mulungu woona ndi kugawa zopereka za Yehova+ ndi zinthu zopatulika koposa.+