Nehemiya 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako, Zadoki+ mwana wamwamuna wa Imeri, anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake. Ndiyeno, Semaya mwana wamwamuna wa Sekaniya, woyang’anira Chipata cha Kum’mawa,+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Zadoki analekezera.
29 Kenako, Zadoki+ mwana wamwamuna wa Imeri, anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yake. Ndiyeno, Semaya mwana wamwamuna wa Sekaniya, woyang’anira Chipata cha Kum’mawa,+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Zadoki analekezera.