1 Mafumu 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 osawerengera golide wochokera kwa amalonda oyendayenda, ndi phindu lochokera kwa amalonda, komanso golide wochokera kwa mafumu onse+ a Aluya,+ ndi kwa abwanamkubwa a m’dzikolo. 1 Mafumu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Panalinso mahatchi amene Solomo anali kugula kuchokera ku Iguputo, ndipo gulu la amalonda a mfumu ndilo linali kugula mahatchiwo m’magulumagulu.+
15 osawerengera golide wochokera kwa amalonda oyendayenda, ndi phindu lochokera kwa amalonda, komanso golide wochokera kwa mafumu onse+ a Aluya,+ ndi kwa abwanamkubwa a m’dzikolo.
28 Panalinso mahatchi amene Solomo anali kugula kuchokera ku Iguputo, ndipo gulu la amalonda a mfumu ndilo linali kugula mahatchiwo m’magulumagulu.+