Deuteronomo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uzipita kwa ansembe+ achilevi ndi kwa woweruza+ amene aziweruza m’masiku amenewo. Uziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuza chigamulo.+ Ezara 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Ezara ananyamuka ndipo anauza atsogoleri a ansembe, a Alevi ndi a Aisiraeli onse kuti alumbire+ kuti achita mogwirizana ndi mawu amenewa. Choncho iwo analumbira.
9 Uzipita kwa ansembe+ achilevi ndi kwa woweruza+ amene aziweruza m’masiku amenewo. Uziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuza chigamulo.+
5 Pamenepo Ezara ananyamuka ndipo anauza atsogoleri a ansembe, a Alevi ndi a Aisiraeli onse kuti alumbire+ kuti achita mogwirizana ndi mawu amenewa. Choncho iwo analumbira.