Salimo 76:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu nonse amene mwazungulira Mulungu, lonjezani ndi kukwaniritsa malonjezo anuwo kwa Yehova Mulungu wanu.+Bweretsani mphatso mwamantha.+ Salimo 119:106 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 106 Ndalumbira kuti ndidzasunga zigamulo zanu zolungama,+Ndipo ndidzakwaniritsa lumbiro langa.+ Mlaliki 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuli bwino kuti usalonjeze+ kusiyana ndi kulonjeza koma osakwaniritsa zimene walonjezazo.+
11 Inu nonse amene mwazungulira Mulungu, lonjezani ndi kukwaniritsa malonjezo anuwo kwa Yehova Mulungu wanu.+Bweretsani mphatso mwamantha.+