-
Machitidwe 8:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Poyankha iye anati: “Ndingamvetse bwanji popanda wondimasulira?” Pamenepo anachonderera Filipo kuti akwere ndi kukhala naye m’galetamo.
-