Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 146:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Nyanja ndi zonse zili mmenemo.+Wosunga choonadi mpaka kalekale.+ Chivumbulutso 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+
6 Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Nyanja ndi zonse zili mmenemo.+Wosunga choonadi mpaka kalekale.+ Chivumbulutso 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+
7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+