Ezara 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ineyo mfumu Aritasasita ndalamula+ asungichuma onse+ amene ali kutsidya lina la Mtsinje,*+ kuti chilichonse chimene wansembe Ezara,+ wokopera chilamulo cha Mulungu wakumwamba, angapemphe kwa inu chichitidwe mwamsanga. Nehemiya 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pake ndinafika kwa abwanamkubwa+ kutsidya lina la Mtsinje ndi kuwapatsa makalata a mfumu. Kuwonjezera apo, mfumu inandipatsa akuluakulu a gulu lankhondo ndi asilikali okwera pamahatchi* kuti ndiyende nawo.
21 “Ineyo mfumu Aritasasita ndalamula+ asungichuma onse+ amene ali kutsidya lina la Mtsinje,*+ kuti chilichonse chimene wansembe Ezara,+ wokopera chilamulo cha Mulungu wakumwamba, angapemphe kwa inu chichitidwe mwamsanga.
9 Pambuyo pake ndinafika kwa abwanamkubwa+ kutsidya lina la Mtsinje ndi kuwapatsa makalata a mfumu. Kuwonjezera apo, mfumu inandipatsa akuluakulu a gulu lankhondo ndi asilikali okwera pamahatchi* kuti ndiyende nawo.