Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamenepo, akalonga+ a nyumba za makolo,+ akalonga+ a mafuko a Aisiraeli, atsogoleri a magulu a anthu 1,000,+ ndi a magulu a anthu 100,+ ndiponso atsogoleri oyang’anira ntchito+ za mfumu, anayamba kupereka zinthu mwa kufuna kwawo.

  • 2 Mbiri 32:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 anagwirizana ndi akalonga ake+ ndi amuna ake amphamvu kuti atseke akasupe a madzi amene anali kunja kwa mzindawo,+ choncho iwo anamuthandiza.

  • Ezara 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho aloleni akalonga+ athu kuti aimire mpingo wonse ndipo anthu onse a m’mizinda yathu amene atenga akazi achilendo, abwere pa nthawi zimene zikhazikitsidwe. Abwere limodzi ndi akulu a mzinda uliwonse ndi oweruza ake, mpaka titathetsa mkwiyo wa Mulungu wathu umene watiyakira pa nkhani imeneyi.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena