1 Mbiri 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa Alevi panali Semaya mwana wa Hasubu. Hasubu anali mwana wa Azirikamu, ndipo Azirikamu anali mwana wa Hasabiya.+ Amenewa anali ochokera kwa ana a Merari.
14 Pa Alevi panali Semaya mwana wa Hasubu. Hasubu anali mwana wa Azirikamu, ndipo Azirikamu anali mwana wa Hasabiya.+ Amenewa anali ochokera kwa ana a Merari.