1 Mbiri 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso panali Obadiya mwana wa Semaya.+ Semaya anali mwana wa Galali, Galali anali mwana wa Yedutuni.+ Ndiye panalinso Berekiya mwana wa Asa mwana wa Elikana, amene anali kukhala m’midzi ya Anetofa.+
16 Komanso panali Obadiya mwana wa Semaya.+ Semaya anali mwana wa Galali, Galali anali mwana wa Yedutuni.+ Ndiye panalinso Berekiya mwana wa Asa mwana wa Elikana, amene anali kukhala m’midzi ya Anetofa.+