Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Anthu amene anabwera kuchokera ku ukapolo,+ amene kale anali m’dziko la eni, anapereka nsembe zopsereza+ kwa Mulungu wa Isiraeli. Anapereka ng’ombe zamphongo 12+ za Aisiraeli onse, nkhosa zamphongo 96,+ ana a nkhosa amphongo 77, ndi mbuzi zamphongo 12+ monga nsembe yamachimo. Zonsezi anazipereka monga nsembe yopsereza kwa Yehova.

  • Yeremiya 52:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 M’chaka cha 23 cha ulamuliro wa Nebukadirezara, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga Ayuda 745 kupita nawo ku ukapolo.+

      Anthu onse amene anawatenga anali 4,600.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena