1 Mbiri 2:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima. 1 Mbiri 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso panali Obadiya mwana wa Semaya.+ Semaya anali mwana wa Galali, Galali anali mwana wa Yedutuni.+ Ndiye panalinso Berekiya mwana wa Asa mwana wa Elikana, amene anali kukhala m’midzi ya Anetofa.+ Nehemiya 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Amuna a ku Betelehemu+ ndi ku Netofa,+ 188.
54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima.
16 Komanso panali Obadiya mwana wa Semaya.+ Semaya anali mwana wa Galali, Galali anali mwana wa Yedutuni.+ Ndiye panalinso Berekiya mwana wa Asa mwana wa Elikana, amene anali kukhala m’midzi ya Anetofa.+