Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ezara anawerenga+ mokweza bukulo m’bwalo lalikulu limene linali pafupi ndi Chipata cha Kumadzi, kuyambira m’mawa+ mpaka masana. Anali kuwerenga bukuli pamaso pa amuna, akazi ndi ana amene akanatha kumvetsera ndi kuzindikira. Anthu onse anatchera khutu kuti amve+ zimene zinali m’buku la chilamuloli.

  • Luka 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Yesu anamufunsa kuti: “Kodi m’Chilamulo analembamo chiyani?+ Umawerengamo zotani?”

  • Machitidwe 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri+ a sunagoge anawatumizira mawu akuti: “Amuna inu, abale athu, ngati muli ndi mawu alionse olimbikitsa nawo anthu, lankhulani.”

  • Machitidwe 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera m’mabuku a Mose, chifukwa mabuku amenewa amawerengedwa mokweza m’masunagoge sabata lililonse.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena