Nehemiya 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chinanso: Kwa zaka 12, kuchokera tsiku limene anandiika kukhala bwanamkubwa wawo+ m’dziko la Yuda, m’chaka cha 20+ mpaka m’chaka cha 32+ cha mfumu Aritasasita,+ ine ndi abale anga sitinadye chakudya choyenera kuperekedwa kwa bwanamkubwa.+
14 Chinanso: Kwa zaka 12, kuchokera tsiku limene anandiika kukhala bwanamkubwa wawo+ m’dziko la Yuda, m’chaka cha 20+ mpaka m’chaka cha 32+ cha mfumu Aritasasita,+ ine ndi abale anga sitinadye chakudya choyenera kuperekedwa kwa bwanamkubwa.+