Esitere 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Moredekai+ analemba zochitika zimenezi ndi kutumiza makalata kwa Ayuda onse amene anali m’zigawo zonse+ za Mfumu Ahasiwero, zakutali ndi zapafupi zomwe.
20 Ndiyeno Moredekai+ analemba zochitika zimenezi ndi kutumiza makalata kwa Ayuda onse amene anali m’zigawo zonse+ za Mfumu Ahasiwero, zakutali ndi zapafupi zomwe.