Ekisodo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mwezi uno uzikhala mwezi wanu woyamba* wa miyezi ya pa chaka. Chaka chanu chiziyamba ndi mwezi uno.+ Ekisodo 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Muzisunga chikondwerero cha mkate wosafufumitsa.+ Monga momwe ndinakulamulirani, muzidya mkate wosafufumitsa masiku 7 m’mwezi wa Abibu*+ pa nthawi yoikidwiratu, chifukwa munatuluka mu Iguputo m’mwezi wa Abibu.
2 “Mwezi uno uzikhala mwezi wanu woyamba* wa miyezi ya pa chaka. Chaka chanu chiziyamba ndi mwezi uno.+
18 “Muzisunga chikondwerero cha mkate wosafufumitsa.+ Monga momwe ndinakulamulirani, muzidya mkate wosafufumitsa masiku 7 m’mwezi wa Abibu*+ pa nthawi yoikidwiratu, chifukwa munatuluka mu Iguputo m’mwezi wa Abibu.