Esitere 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Poyankha Esitere anati: “Munthu wake ndi uyu, Hamani, mdani ndiponso munthu woipa.”+ Pamenepo Hamani anachita mantha+ chifukwa cha mfumu ndi mfumukazi. Esitere 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Izi zinali choncho chifukwa Hamani+ mwana wa Hamedata+ Mwagagi,+ amene anali kudana+ ndi Ayuda onse, anakonzera Ayudawo chiwembu kuti awawononge.+ Choncho iye anachita Puri+ kapena kuti Maere,+ ndi cholinga chakuti awasautse ndi kuwawononga.
6 Poyankha Esitere anati: “Munthu wake ndi uyu, Hamani, mdani ndiponso munthu woipa.”+ Pamenepo Hamani anachita mantha+ chifukwa cha mfumu ndi mfumukazi.
24 Izi zinali choncho chifukwa Hamani+ mwana wa Hamedata+ Mwagagi,+ amene anali kudana+ ndi Ayuda onse, anakonzera Ayudawo chiwembu kuti awawononge.+ Choncho iye anachita Puri+ kapena kuti Maere,+ ndi cholinga chakuti awasautse ndi kuwawononga.