Esitere 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ngati zingakukomereni mfumu, palembedwe makalata kuti anthu amenewa awonongedwe. Ine ndidzapereka matalente 10,000+ asiliva kwa anthu amene adzagwira ntchito imeneyi+ kuti abweretse matalentewo mosungiramo chuma cha mfumu.”
9 Ngati zingakukomereni mfumu, palembedwe makalata kuti anthu amenewa awonongedwe. Ine ndidzapereka matalente 10,000+ asiliva kwa anthu amene adzagwira ntchito imeneyi+ kuti abweretse matalentewo mosungiramo chuma cha mfumu.”