Salimo 94:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi inu mudzagwirizana ndi olamulira ankhanza,+Pamene akuyambitsa mavuto mwa kupanga malamulo?+ Danieli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya,+ amene sasintha.”+
8 Tsopano inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya,+ amene sasintha.”+