Esitere 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Esitere anaitana Hataki,+ mmodzi mwa amuna ofulidwa a mfumu amene mfumuyo inamuika kuti azitumikira Esitere. Ndiyeno anamutumiza kwa Moredekai kuti akafufuze zimene zachitika.
5 Pamenepo Esitere anaitana Hataki,+ mmodzi mwa amuna ofulidwa a mfumu amene mfumuyo inamuika kuti azitumikira Esitere. Ndiyeno anamutumiza kwa Moredekai kuti akafufuze zimene zachitika.