Hoseya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo pamapeto pake anapambana.+ Analira pochonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli+ ndipo kumeneko Mulungu anayamba kulankhula nafe.+ Luka 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndikukuuzani, Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna,+ ndipo mudzapeza. Gogodanibe, ndipo adzakutsegulirani.
4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo pamapeto pake anapambana.+ Analira pochonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli+ ndipo kumeneko Mulungu anayamba kulankhula nafe.+
9 Choncho ndikukuuzani, Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna,+ ndipo mudzapeza. Gogodanibe, ndipo adzakutsegulirani.