Genesis 32:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthuyo ataona kuti Yakobo sakugonja,+ anamugwira nsukunyu* yake, ndipo nsukunyuyo inaguluka polimbana naye.+
25 Munthuyo ataona kuti Yakobo sakugonja,+ anamugwira nsukunyu* yake, ndipo nsukunyuyo inaguluka polimbana naye.+