Esitere 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mfumukazi Vasiti inakana+ kubwera itaitanidwa ndi mfumu kudzera mwa nduna za panyumba ya mfumu. Pamenepo mfumu inakwiya kwambiri ndipo mumtima mwake munali ukali waukulu.+
12 Koma Mfumukazi Vasiti inakana+ kubwera itaitanidwa ndi mfumu kudzera mwa nduna za panyumba ya mfumu. Pamenepo mfumu inakwiya kwambiri ndipo mumtima mwake munali ukali waukulu.+